Maliro 5:10 - Buku Lopatulika10 Khungu lathu lapserera ngati pamoto chifukwa cha kuwawa kwa njala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Khungu lathu lapserera ngati pamoto chifukwa cha kuwawa kwa njala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Khungu lathu likutentha ngati lili m'ng'anjo chifukwa cha ululu wa njala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Khungu lathu latentha ngati uvuni mʼngʼanjo, chifukwa cha kuwawa kwa njala. Onani mutuwo |