Maliro 4:8 - Buku Lopatulika8 Maonekedwe ao ada koposa makala, sazindikirika m'makwalala; khungu lao limamatira pa mafupa ao, lakhwinyata, lasanduka ngati ndodo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Maonekedwe ao ada koposa makala, sazindikirika m'makwalala; khungu lao limamatira pa mafupa ao, lakhwinyata, lasanduka ngati ndodo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Koma tsopano nkhope zao zasanduka zakuda ngati mwaye. Palibe amene akuŵazindikira m'miseu. Khungu lao lachita makwinyamakwinya, langoti gwa ngati mtengo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Koma tsopano maonekedwe awo ndi akuda kuposa mwaye; palibe angawazindikire mʼmisewu ya mu mzinda. Khungu lawo lachita makwinyamakwinya pa mafupa awo; lawuma gwaa ngati nkhuni. Onani mutuwo |