Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Maliro 4:5 - Buku Lopatulika

5 Omwe anadya zolongosoka angosiyidwa m'makwalala; omwe analeredwa navekedwa mlangali afungatira madzala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Omwe anadya zolongosoka angosiyidwa m'makwalala; omwe analeredwa navekedwa mlangali afungatira madzala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Amene ankadya zokoma akuthera m'miseu. Amene ankavala zokongola zokhazokha tsopano ali gone pa dzala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Iwo amene kale ankadya zonona akupemphetsa mʼmisewu ya mu mzinda. Iwo amene kale ankavala zokongola tsopano akugona pa phulusa.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 4:5
17 Mawu Ofanana  

Ana aakazi inu a Israele, mulirire Saulo, amene anakuvekani ndi zofiira zokometsetsa, amene anaika zokometsetsa zagolide pa zovala zanu.


Koma kazembeyo ananena nao, Ngati mbuyanga ananditumiza kwa mbuyako, ndi kwa iwe, kunena mau awa? Si kwa anthu awa nanga okhala palinga, kuti akadye zonyansa zao, ndi kumwa mkodzo wao pamodzi ndi inu?


Avumbwa ndi mvula kumapiri, nafukata thanthwe posowa pousapo.


Saopera banja lake chipale chofewa; pakuti banja lake lonse livala mlangali.


Anthu ake onse ausa moyo nafunafuna mkate; ndi zokondweretsa zao agula zakudya kuti atsitsimutse moyo wao; taonani, Yehova, nimupenye; pakuti ndasanduka wonyansa.


Ndipo analakalaka kukhutitsa mimba yake ndi makoko amene nkhumba zimadya, ndipo palibe munthu anamninkha kanthu.


Ndipo panali munthu mwini chuma amavala chibakuwa ndi nsalu yabafuta, nasekera, nadyerera masiku onse;


Koma munatuluka kukaona chiyani? Munthu wovala zovala zofewa kodi? Onani, iwo akuvala zolemera, ndi akukhala odyerera, ali m'nyumba za mafumu.


Koma iye wakutsata zomkondweretsa, adafa pokhala ali ndi moyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa