Maliro 4:18 - Buku Lopatulika18 Amalondola mapazi athu, sitingayende m'makwalala athu; chitsiriziro chathu chayandikira, masiku athu akwaniridwa; pakuti chitsiriziro chathu chafikadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Amalondola mapazi athu, sitingayende m'makwalala athu; chitsiriziro chathu chayandikira, masiku athu akwaniridwa; pakuti chitsiriziro chathu chafikadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Anthu ankangotilondola nthaŵi zonse, kotero kuti sitinkathanso kuyenda m'miseu yathu. Masiku athu ankacheperachepera, imfa yathu idaayandikira, ndithu chimalizo chinali chitafika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Anthu ankalondola mapazi athu, choncho sitikanayenda mʼmisewu yathu mu mzinda. Chimaliziro chathu chinali pafupi, masiku athu anali owerengeka, chifukwa chimaliziro chathu chinali chitafika. Onani mutuwo |