Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Maliro 4:12 - Buku Lopatulika

12 Mafumu a dziko lapansi sanakhulupirire, ngakhale onse okhala kunja kuno, kuti adani ndi amaliwongo adzalowadi m'zipata za Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Mafumu a dziko lapansi sanakhulupirire, ngakhale onse okhala kunja kuno, kuti adani ndi amaliwongo adzalowadi m'zipata za Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Mafumu a pa dziko lapansi sadakhulupirire, kapena wina aliyense wokhala pa dziko lapansi, kuti adani kapena ankhondo nkuloŵa pa zipata za Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Mafumu a pa dziko lapansi sanakhulupirire, kapena wina aliyense wokhala pa dziko lonse, kuti adani kapena ankhondo akhoza kulowa pa zipata za Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 4:12
5 Mawu Ofanana  

Ndipo mwezi wachisanu, tsiku lachisanu ndi chiwiri la mweziwo, ndicho chaka chakhumi mphambu chisanu ndi chinai cha mfumu Nebukadinezara mfumu ya Babiloni, Nebuzaradani mkulu wa olindirira, ndiye mnyamata wa mfumu ya Babiloni, anadza ku Yerusalemu,


Taonani, Ine ndine mdani wako, iwe wokhala m'chigwa, ndi pa thanthwe la m'chidikha, ati Yehova; inu amene muti, Ndani adzatsikira kumenyana ndi ife? Ndani adzalowa m'zokhalamo zathu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa