Maliro 4:1 - Buku Lopatulika1 Ha! Golide wagugadi; golide woona woposa wasandulika; miyala ya malo opatulika yakhuthulidwa pa malekezero a makwalala onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ha! Golide wagugadi; golide woona woposa wasandulika; miyala ya malo opatulika yakhuthulidwa pa malekezero a makwalala onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ha! Golide wathu tsopano wathimbirira kwambiri. Golide wathu wosalala uja wasinthika kotheratu. Miyala ya ku malo oyera yamwazikana, ili vuu, ku mphambano zonse za miseu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Haa! Golide wathimbirira, golide wosalala wasinthikiratu! Amwazamwaza miyala yokongola ya kumalo opatulika pamphambano ponse pa mzinda. Onani mutuwo |