Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Maliro 3:9 - Buku Lopatulika

9 Watsekereza njira zanga ndi miyala yosema, nakhotetsa mayendedwe anga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Watsekereza njira zanga ndi miyala yosema, nakhotetsa mayendedwe anga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Adanditsekera mseu ndi miyala yosema, ndipo adakhotetsa njira zanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Wanditsekera njira yanga ndi miyala yosema; ndipo wakhotetsa tinjira tanga.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 3:9
6 Mawu Ofanana  

Iye ananditsekera njira kuti ndisapitireko, naika mdima poyendapo ine.


ndi mpweya wake uli ngati mtsinje wosefukira, umene ufikira m'khosi, kupeta mitundu ya anthu ndi chopetera cha chionongeko; ndi chapakamwa chalakwitsa, chidzakhala m'nsagwada za anthu.


Yehova bwanji mwatisocheretsa kusiya njira zanu, ndi kuumitsa mitima yathu tisakuopeni? Bwerani, chifukwa cha atumiki anu, mafuko a cholowa chanu.


Andikhalira chilombo cholalira kapena mkango mobisalira.


Wapambutsa njira zanga, nanding'amba; nandipululutsa.


Chifukwa chake taonani, ndidzatchinga njira yako ndi minga, ndipo ndidzammangira mpanda, kuti asapeze mabande ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa