Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Maliro 3:8 - Buku Lopatulika

8 Inde, pofuula ine ndi kuitana andithandize amakaniza pemphero langa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Inde, pofuula ine ndi kuitana andithandize amakaniza pemphero langa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Ngakhale pamene ndinkafuula ndi kupempha chithandizo, sankalimva pemphero langalo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ngakhale pamene ndifuwula kapena kupempha chithandizo, amakana pemphero langa.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 3:8
9 Mawu Ofanana  

Taonani, ndifuula kuti, Chiwawa! Koma sandimvera; ndikuwa, koma palibe chiweruzo.


Ndifuula kwa Inu, koma simundiyankha; ndinyamuka, ndipo mungondipenyerera.


Mulungu wanga, ndiitana usana, koma simuvomereza; ndipo usiku, sindikhala chete.


Yehova, Mulungu wa makamu, mudzakwiyira pemphero la anthu anu kufikira liti?


Mwadzikuta ndi mkwiyo ndi kutilondola, mwatipha osachitira chisoni.


Mwadzikuta ndi mtambo kuti pemphero lathu lisapyolemo.


Yehova, ndidzafuula mpaka liti osamva Inu? Ndifuulira kwa Inu za chiwawa, koma simupulumutsa.


Ndipo poyandikira ora lachisanu ndi chinai, Yesu anafuula ndi mau aakulu, kunena, Eli, Eli, lama sabakitani? ndiko kunena kuti, Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji Ine?


Pakuti yense wakupempha alandira; ndi wofunayo apeza; ndi iye amene agogoda adzamtsegulira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa