Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Maliro 3:6 - Buku Lopatulika

6 Wandikhalitsa mumdima ngati akufa kale.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Wandikhalitsa mumdima ngati akufa kale.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Adanditaya m'malo a mdima wabii, kuti ndikhale ngati munthu wofa kalekale.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Wandikhazika mu mdima ngati amene anafa kale.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 3:6
4 Mawu Ofanana  

Pakuti mdani alondola moyo wanga; apondereza pansi moyo wanga; andikhalitsa mumdima monga iwo adafa kale lomwe.


Fulumirani ndiyankheni, Yehova; mzimu wanga ukutha. Musandibisire nkhope yanu; ndingafanane nao akutsikira kudzenje.


Tiyambasira khoma ngati wakhungu, inde tiyambasa monga iwo opanda maso; tiphunthwa usana monga m'chizirezire; tili m'malo amdima ngati akufa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa