Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Maliro 3:54 - Buku Lopatulika

54 madzi anayenda pamwamba pamutu panga, ndinati, Ndalikhidwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

54 madzi anayenda pamwamba pa mutu panga, ndinati, Ndalikhidwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

54 Madzi adaamiza mutu wanga, ine nkunena ku, “Mayo, ndikufa ine!”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

54 madzi anamiza mutu wanga ndipo ndinkaganiza kuti imfa yayandikira.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 3:54
15 Mawu Ofanana  

kapena mdima kuti ungaone, ndi madzi aunyinji akumiza.


Zingwe za imfa zinandizinga, ndipo mitsinje ya zopanda pake inandiopsa.


Ndipo ine, pakutenga nkhawa, ndinati, Ndadulidwa kundichotsa pamaso panu. Komatu munamva mau a kupemba kwanga pamene ndinafuulira kwa Inu.


Chigumula chisandifotsere, ndipo chakuya chisandimize; ndipo asanditsekere pakamwa pake pa dzenje.


Kuzaza kwanu kwandimiza; zoopsa zanu zinandiononga.


Anachotsedwa ku chipsinjo ndi chiweruziro; ndipo ndani adzafotokoza nthawi ya moyo wake? Pakuti walikhidwa kunja kuno; chifukwa cha kulakwa kwa anthu anga Iye anakhomedwa.


Ndipo ndinati, Mphamvu yanga yatha, osayembekezanso kanthu kwa Yehova.


Pamenepo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, Mafupa awa ndiwo nyumba yonse ya Israele; taonani, akuti, Mafupa athu auma, chiyembekezo chathu chatayika, talikhidwa.


Pakuti yense wakupempha alandira; ndi wofunayo apeza; ndi iye amene agogoda adzamtsegulira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa