Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Maliro 3:41 - Buku Lopatulika

41 Titukulire mitima yathu ndi manja athu omwe kwa Mulungu ali kumwamba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 Titukulire mitima yathu ndi manja athu omwe kwa Mulungu ali kumwamba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 Tikweze mitima yathu ndi manja athu kwa Mulungu kumwamba.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 Tiyeni tikweze mitima yathu ndi manja athu kwa Mulungu kumwamba ndipo tinene kuti:

Onani mutuwo Koperani




Maliro 3:41
10 Mawu Ofanana  

Ukakonzeratu mtima wako, ndi kumtambasulira Iye manja ako;


Kwezani manja anu kumalo oyera, nimulemekeze Yehova.


Pemphero langa liikike ngati chofukiza pamaso panu; kukweza manja anga kuikike ngati nsembe ya madzulo.


Ndikweza moyo wanga kwa Inu, Yehova.


Mverani mau a kupemba kwanga, pamene ndilirira Inu, pamene ndikweza manja anga kuloza ponenera panu poyera.


Potero ndidzakuyamikani m'moyo mwanga; ndidzakweza manja anga m'dzina lanu.


Kondwetsani moyo wa mtumiki wanu; pakuti ndikwezera moyo wanga kwa Inu, Ambuye.


Pakuti atero Iye amene ali wamtali wotukulidwa, amene akhala mwachikhalire, amene dzina lake ndiye Woyera, Ndikhala m'malo aatali ndi oyera, pamodzi ndi yense amene ali wa mzimu wosweka ndi wodzichepetsa, kutsitsimutsa mzimu wa odzichepetsa, ndi kutsitsimutsa mtima wa osweka.


kotero ife poliralira inu, tinavomera mokondwera kupereka kwa inu si Uthenga Wabwino wa Mulungu wokha, komanso moyo wathu, popeza mudakhala okondedwa kwa ife.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa