Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Maliro 3:18 - Buku Lopatulika

18 Ndipo ndinati, Mphamvu yanga yatha, osayembekezanso kanthu kwa Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ndipo ndinati, Mphamvu yanga yatha, osayembekezanso kanthu kwa Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Choncho ndikuti, “Ulemerero wanga wonse watha, chandithera chikhulupiriro cholandira kanthu ka Chauta.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Choncho ndikuti, “Ulemerero wanga wachoka ndi zonse zimene ndimayembekeza kwa Yehova.”

Onani mutuwo Koperani




Maliro 3:18
7 Mawu Ofanana  

chilikuti chiyembekezo changa? Inde, chiyembekezo changa adzachiona ndani?


Mphamvu yanga njotani kuti ndiyembekeze? Mathedwe anga ndi otani kuti ndipirire?


Pofulumizidwa mtima ndinati ine, anthu onse nga mabodza.


Ndipo ine, pakutenga nkhawa, ndinati, Ndadulidwa kundichotsa pamaso panu. Komatu munamva mau a kupemba kwanga pamene ndinafuulira kwa Inu.


Pamenepo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, Mafupa awa ndiwo nyumba yonse ya Israele; taonani, akuti, Mafupa athu auma, chiyembekezo chathu chatayika, talikhidwa.


Pakuti yense wakupempha alandira; ndi wofunayo apeza; ndi iye amene agogoda adzamtsegulira.


Ndipo Davide ananena mumtima mwake, Tsiku lina Saulo adzandipha; palibe china chondikomera koma kuti ndithawire ku dziko la Afilisti; ndipo Saulo adzakhala kakasi chifukwa cha ine, osandifunanso m'malire onse a Israele, momwemo ndidzapulumuka m'dzanja lake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa