Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 9:25 - Buku Lopatulika

25 koma ophunzira ake anamtenga usiku, nampyoletsa palinga, namtsitsa mu dengu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 koma ophunzira ake anamtenga usiku, nampyoletsa palinga, namtsitsa mu dengu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Koma ophunzira ake adamtenga usiku, namtsitsira kunja kwa lingalo m'dengu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Koma ophunzira ake anamutenga usiku, namutsitsira kunja kwa mpandawo mʼdengu.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 9:25
7 Mawu Ofanana  

Ndipo onsewa anadya, nakhuta: ndipo anatola makombo otsala madengu asanu ndi awiri odzala.


Ndipo ophunzira, yense monga anakhoza, anatsimikiza mtima kutumiza zothandiza abale akukhala mu Yudeya;


koma chiwembu chao chinadziwika ndi Saulo. Ndipo anadikiranso pazipata usana ndi usiku kuti amuphe;


Koma m'mene anafika ku Yerusalemu, anayesa kudziphatika kwa ophunzira; ndipo anamuopa iye onse, osakhulupirira kuti ali wophunzira.


ndipo mwa zenera, mudengu, ananditsitsa pakhoma, ndipo ndinapulumuka m'manja mwake.


Pamenepo anawatsitsa pazenera ndi chingwe; popeza nyumba yake inali pa linga la mzinda, nakhala iye palingapo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa