Machitidwe a Atumwi 8:28 - Buku Lopatulika28 ndipo analinkubwerera, nalikukhala pa galeta wake, nawerenga mneneri Yesaya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 ndipo analinkubwerera, nalikukhala pa galeta wake, nawerenga mneneri Yesaya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Nthaŵi imeneyo ankabwerera kwao. Anali pa galeta akuŵerenga buku la mneneri Yesaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 ndipo akubwerera kwawo atakwera pa galeta lake amawerenga buku la mneneri Yesaya. Onani mutuwo |