Machitidwe a Atumwi 8:19 - Buku Lopatulika19 nanena, Ndipatseni inenso ulamuliro umene, kuti aliyense amene ndikaika manja pa iye, alandire Mzimu Woyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 nanena, Ndipatseni inenso ulamuliro umene, kuti amene aliyense ndikaika manja pa iye, alandire Mzimu Woyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Adati, “Bwanji mutandipatsako inenso mphamvu imeneyi, kuti aliyense amene ndikamsanjike manja, akalandire Mzimu Woyera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 “Inenso ndipatseni mphamvu imeneyi kuti aliyense amene ndimusanjika manja anga azilandira Mzimu Woyera.” Onani mutuwo |