Machitidwe a Atumwi 8:18 - Buku Lopatulika18 Koma pakuona Simoni kuti mwa kuika manja a atumwi anapatsidwa Mzimu Woyera, anawatengera ndalama, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Koma pakuona Simoni kuti mwa kuika manja a atumwi anapatsidwa Mzimu Woyera, anawatengera ndalama, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Simoni uja ataona kuti Mzimu Woyera waperekedwa kwa iwo atumwi aja ataŵasanjika manja, adafuna kuŵapatsa ndalama atumwiwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Simoni ataona kuti Mzimu anaperekedwa kwa iwo atumwi atawasanjika manja, iye anafuna kuwapatsa ndalama ndipo anati, Onani mutuwo |