Machitidwe a Atumwi 8:15 - Buku Lopatulika15 amenewo, m'mene adatsikirako, anawapempherera, kuti alandire Mzimu Woyera: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 amenewo, m'mene adatsikirako, anawapempherera, kuti alandire Mzimu Woyera: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Iwowo atafika, adayamba kupempherera okhulupirira aja kuti alandire Mzimu Woyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Atafika anawapempherera kuti alandire Mzimu Woyera, Onani mutuwo |