Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 8:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo anamsamalira iye, popeza nthawi yaikulu adawadabwitsa iwo ndi matsenga ake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo anamsamalira iye, popeza nthawi yaikulu adawadabwitsa iwo ndi matsenga ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ankamutsata chifukwa pa nthaŵi yaitali ankaŵadodometsa ndi matsenga akewo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Anthu amamutsata chifukwa kwa nthawi yayitali amawadabwitsa ndi matsenga akewo.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 8:11
6 Mawu Ofanana  

Ndine amene nditsutsa zizindikiro za matukutuku, ndi kuchititsa misala oombeza ula; ndi kubwezera m'mbuyo anthu anzeru, ndi kupusitsa nzeru zao:


Ndipo pamene iwo adzati kwa iwe, Funa kwa olaula, ndi obwebweta, amene alira pyepye, nang'ung'udza; kodi anthu sadzafuna kwa Mulungu wao? Chifukwa cha amoyo, kodi adzafuna kwa akufa?


Ndipo m'mene anapitirira chisumbu chonse kufikira Pafosi, anapezapo munthu watsenga, mneneri wonyenga, ndiye Myuda, dzina lake Barayesu;


Koma panali munthu dzina lake Simoni amene adachita matsenga m'mzindamo kale, nadabwitsa anthu a Samariya, ndi kunena kuti iye yekha ndiye munthu wamkulu;


Agalatiya opusa inu, anakulodzani ndani, inu amene Yesu Khristu anaonetsedwa pamaso panu, wopachikidwa?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa