Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 7:31 - Buku Lopatulika

31 Koma Mose pakuona, anazizwa pa choonekacho; ndipo pakuyandikira iye kukaona, kunadza mau a Ambuye,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Koma Mose pakuona, anazizwa pa choonekacho; ndipo pakuyandikira iye kukaona, kunadza mau a Ambuye,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Mose ataona zimenezi adazizwa, ndipo adasendera pafupi kuti aonetsetse. Pamenepo adamva mau a Chauta akuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Iye ataona zimenezi, anadabwa. Akupita kuti akaonetsetse pafupi, Mose anamva mawu a Ambuye:

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 7:31
4 Mawu Ofanana  

Ndipo pakumva ichi, Yesu anazizwa, nati kwa iwo akumtsata, Indetu ndinena kwa inu, ngakhale mwa Israele, sindinapeze chikhulupiriro chotere.


Ndipo zitapita zaka makumi anai, anamuonekera mngelo m'chipululu cha Sinai, m'lawi la moto wa m'chitsamba.


akuti, Ine ndine Mulungu wa makolo anu, Mulungu wa Abrahamu, ndi wa Isaki, ndi wa Yakobo. Ndipo Mose ananthunthumira, osalimbika mtima kupenyetsako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa