Machitidwe a Atumwi 7:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo Mose anathawa pa mau awa, nakhala mlendo m'dziko la Midiyani; kumeneko anabala ana aamuna awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo Mose anathawa pa mau awa, nakhala mlendo m'dziko la Midiyani; kumeneko anabala ana amuna awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Pamene Mose adamva mau ameneŵa, adathaŵa namakakhala ku chilendo ku dziko la Midiyani. Kumeneko adabereka ana aamuna aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Mose atamva mawu awa anathawira ku Midiyani, kumene anakhala mlendo ndipo anabereka ana amuna awiri. Onani mutuwo |