Machitidwe a Atumwi 7:28 - Buku Lopatulika28 Kodi ufuna kundipha ine, monga muja unapha Mwejipito dzulo? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Kodi ufuna kundipha ine, monga muja unapha Mwejipito dzulo? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Kodi ukufuna kuphanso ine monga udaphera Mwejipito dzulo lija?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Kodi ukufuna kundipha monga momwe unaphera Mwigupto uja dzulo?’ Onani mutuwo |