Machitidwe a Atumwi 7:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo m'mawa mwake anawaonekera alikulimbana ndeu, ndipo anati awateteze, ayanjanenso, nati, Amuna inu, muli abale; muchitirana choipa bwanji? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo m'mawa mwake anawaonekera alikulimbana ndeu, ndipo anati awateteze, ayanjanenso, nati, Amuna inu, muli abale; muchitirana choipa bwanji? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 M'maŵa mwake atabwera, adapeza Aisraele aŵiri akumenyana. Adayesa kuŵayanjanitsa pakuŵauza kuti, ‘Anthuni, muli pa chibale, bwanji mukuvutana?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Mmawa mwake Mose anaona Aisraeli awiri akukangana. Iye anayesa kuwayanjanitsa ponena kuti, ‘Amuna inu, ndinu abale; chifukwa chiyani mukufuna kupwetekana?’ Onani mutuwo |