Machitidwe a Atumwi 7:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo pakuona wina woti alikumchitira choipa, iye anamtchinjiriza, nambwezera chilango wozunzayo, nakantha Mwejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo pakuona wina woti alikumchitira choipa, iye anamtchinjiriza, nambwezera chilango wozunzayo, nakantha Mwejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Tsono pamene adaona kuti Mwejipito wina akuzunza mmodzi mwa abale akewo, Moseyo adatchinjiriza Mwisraeleyo, nalipsira Mwejipito uja pakumupha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Iye ataona mmodzi wa iwo akuzunzidwa ndi Mwigupto, anatchinjiriza Mwisraeliyo, namupha Mwiguptoyo. Onani mutuwo |