Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 5:23 - Buku Lopatulika

23 nanena, Nyumba yandende tinapeza chitsekere, ndi alonda alikuimirira pamakomo; koma pamene tinatsegula sitinapezamo mmodzi yense.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 nanena, Nyumba yandende tinapeza chitsekere, ndi alonda alikuimirira pamakomo; koma pamene tinatsegula sitinapezamo mmodzi yense.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Adati, “Takapeza ndende ili chitsekere ndithu, ndipo alonda ali chilili pa makomo, koma titatsekula zitseko, sitidapezemo munthu.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 kuti, “Tinakapeza ndende ili chitsekere ndithu, ndi alonda atayimirira pa khomo, koma pamene tinatsekula zitseko, sitinapezemo munthu aliyense mʼkatimo.”

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 5:23
13 Mawu Ofanana  

Wokhala m'mwambayo adzaseka; Ambuye adzawanyoza.


Yehova aphwanya upo wa amitundu, asandutsa chabe zolingirira za mitundu ya anthu.


Kulibe nzeru ngakhale luntha ngakhale uphungu wotsutsana ndi Yehova.


Ndani anganene, chonena chake ndi kuchitikadi, ngati Ambuye salamulira?


Pamenepo anatola miyala kuti amponye Iye; koma Yesu anabisala, natuluka mu Kachisi.


Koma mngelo wa Ambuye anatsegula pakhomo pa ndende usiku, nawatulutsa, nati,


Koma anyamata amene adafikako sanawapeze m'ndende, ndipo pobwera anafotokoza,


Koma m'mene anamva mau awa mdindo wa Kachisi ndi ansembe aakulu anathedwa nzeru ndi iwo aja, kuti ichi chidzatani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa