Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 5:22 - Buku Lopatulika

22 Koma anyamata amene adafikako sanawapeze m'ndende, ndipo pobwera anafotokoza,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Koma anyamata amene adafikako sanawapeza m'ndende, ndipo pobwera anafotokoza,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Koma pamene anthuwo adafika kundendeko, sadaŵapezemo. Adabwerako nadzaŵafotokozera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Koma alonda aja atafika kundende, sanawapezemo. Iwo anabwerera nakawafotokozera

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 5:22
4 Mawu Ofanana  

Koma Petro anamtsata kutali, kufikira kubwalo la mkulu wa ansembe, nalowamo, nakhala pansi ndi anyamata, kuti aone chimaliziro.


Koma kutacha, panali phokoso lalikulu mwa asilikali, Petro wamuka kuti.


nanena, Nyumba yandende tinapeza chitsekere, ndi alonda alikuimirira pamakomo; koma pamene tinatsegula sitinapezamo mmodzi yense.


Pamenepo anachoka mdindo pamodzi ndi anyamata; anadza nao, koma osawagwiritsa, pakuti anaopa anthu, angaponyedwe miyala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa