Machitidwe a Atumwi 5:18 - Buku Lopatulika18 nathira manja atumwi, nawaika m'ndende ya anthu wamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 nathira manja atumwi, nawaika m'ndende ya anthu wamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adagwira atumwi aja, naŵatsekera m'ndende ya Boma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Iwo anagwira atumwi ndi kuwatsekera mʼndende ya anthu wamba. Onani mutuwo |