Machitidwe a Atumwi 4:17 - Buku Lopatulika17 Komatu tiwaopse asalankhulenso m'dzina ili kwa munthu aliyense, kuti chisabukenso kwa anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Komatu tiwaopse asalankhulenso m'dzina ili kwa munthu aliyense, kuti chisabukenso kwa anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Koma kuwopa kuti mbiriyi ingaŵande ponseponse, tiyeni tiwachenjeze moopseza kuti polankhula ndi munthu aliyense asatchulenso dzina la Yesu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Koma kuti mbiriyi isapitirire kuwanda pakati pa anthu, ife tiwachenjeze anthu amenewa kuti asayankhulenso kwa wina aliyense mʼdzina la Yesu.” Onani mutuwo |