Machitidwe a Atumwi 4:15 - Buku Lopatulika15 Koma pamene anawalamulira iwo achoke m'bwalo la akulu a milandu, ananena wina ndi mnzake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Koma pamene anawalamulira iwo achoke m'bwalo la akulu, ananena wina ndi mnzake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Choncho adaŵalamula kuti atuluke m'bwalo la milandu lija, kenaka abwalowo adayamba kukambirana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Chifukwa chake anawalamula kuti atuluke mʼbwalo la milandu ndipo akulu abwalowo anayamba kukambirana. Onani mutuwo |