Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 28:5 - Buku Lopatulika

5 Koma anakutumulira chilombocho kumoto, osamva kupweteka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Koma anakutumulira chilombocho kumoto, osamva kupweteka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Komabe Paulo adaikutumulira pa moto njokayo, osapwetekedwa konse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Koma Paulo anayikutumulira pa moto njokayo, ndipo sanamve kupweteka.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 28:5
8 Mawu Ofanana  

Udzaponda mkango ndi mphiri; udzapondereza msona wa mkango ndi chinjoka.


adzatola njoka, ndipo ngakhale akamwa kanthu kakufa nako, sikadzawapweteka; adzaika manja ao pa odwala, ndipo adzachira.


Taonani, ndakupatsani ulamuliro wakuponda pa njoka ndi zinkhanira, ndi pa mphamvu iliyonse ya mdaniyo; ndipo kulibe kanthu kadzakuipsani konse.


Koma anayesa kuti adzatupa, kapena mwini wake kugwa kufa pomwepo; koma m'mene adalindira nthawitu, naona kuti sanapweteke konse, anasintha maganizo, nati, Ndiye Mulungu.


Ndipo Mulungu wa mtendere adzaphwanya Satana pansi pa mapazi anu tsopano lino. Chisomo cha Ambuye wathu Yesu Khristu chikhale ndi inu nonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa