Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 28:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo titapulumuka, pamenepo tinadziwa kuti chisumbucho chinatchedwa Melita.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo titapulumuka, pamenepo tinadziwa kuti chisumbucho chinatchedwa Melita.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Titapulumuka choncho, tidamva kuti chilumbacho dzina lake ndi Melita.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Titapulumuka choncho, tinamva kuti chilumbacho chimatchedwa Melita.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 28:1
6 Mawu Ofanana  

Ndipo m'mene anapitirira chisumbu chonse kufikira Pafosi, anapezapo munthu watsenga, mneneri wonyenga, ndiye Myuda, dzina lake Barayesu;


Pamene anaona masomphenyawo, pomwepo tinayesa kutulukira kunka ku Masedoniya, poganizira kuti Mulungu anaitanira ife kulalikira Uthenga Wabwino kwa iwo.


Ndipo pamene padatsimikizika kuti tipite m'ngalawa kunka ku Italiya, anapereka Paulo ndi andende ena kwa kenturiyo dzina lake Julio, wa gulu la Augusto.


Koma tiyenera kutayika pa chisumbu chakuti.


Ndipo kutacha sanazindikire dzikolo; koma anaona pali bondo la mchenga; kumeneko anafuna, ngati nkutheka, kuyendetsako ngalawa.


ndipo otsalawo, ena pamatabwa, ndi ena pa zina za m'ngalawa. Ndipo kudatero kuti onse adapulumukira pamtunda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa