Machitidwe a Atumwi 27:44 - Buku Lopatulika44 ndipo otsalawo, ena pamatabwa, ndi ena pa zina za m'ngalawa. Ndipo kudatero kuti onse adapulumukira pamtunda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 ndipo otsalawo, ena pamatabwa, ndi ena pa zina za m'ngalawa. Ndipo kudatero kuti onse adapulumukira pamtunda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Otsalawo adaŵalamula kuti agwire matabwa kapena zina za chombo choswekacho. Motero onse adapulumuka nakafika kumtunda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Otsalawo anayenera kugwira matabwa kapena tizidutswa ta sitimayo. Motero onse anapulumuka nakafika pa mtunda. Onani mutuwo |