Machitidwe a Atumwi 27:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo kutacha sanazindikire dzikolo; koma anaona pali bondo la mchenga; kumeneko anafuna, ngati nkutheka, kuyendetsako ngalawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo kutacha sanazindikira dzikolo; koma anaona pali bondo la mchenga; kumeneko anafuna, ngati nkutheka, kuyendetsako ngalawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Kutacha, anthu sadazindikire mtundawo, koma adaona bondo la nyanja lamchenga. Tsono adaganiza kuti ngati nkotheka, akakocheze chombo kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Kutacha, anthu sanazindikire dzikolo, koma anaona pomwe sitima zimayimapo pamodzi ndi mchenga wa pa gombe. Iwo anaganiza zokocheza sitimayo kumeneko ngati zikanatheka kutero. Onani mutuwo |