Machitidwe a Atumwi 27:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo anakhala olimbika mtima onse, natenga chakudya iwo omwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo anakhala olimbika mtima onse, natenga chakudya iwo omwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Pamenepo onse aja adalimba mtima, iwonso nkuyamba kudya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Onse analimba mtima nayamba kudyanso. Onani mutuwo |