Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 27:32 - Buku Lopatulika

32 Pamenepo asilikali anadula zingwe za bwato, naligwetsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Pamenepo asilikali anadula zingwe za bwato, naligwetsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Pamenepo asilikali aja adadula zingwe za kabwato kaja nakaleka kuti kagwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Pamenepo asilikaliwo anadula zingwe za bwatolo ndipo linagwera mʼmadzi.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 27:32
5 Mawu Ofanana  

Ndipo mbuye wake anatama kapitao wonyengayo, kuti anachita mwanzeru; chifukwa ana a nthawi ya pansi pano ali anzeru m'mbadwo wao koposa ana a kuunika.


Ndipo pamene adapanga mkwapulo wazingwe, anatulutsa onse mu Kachisimo, ndi nkhosa ndi ng'ombe; nakhuthula ndalama za osinthanawo, nagubuduza magome;


Paulo anati kwa kenturiyo ndi kwa asilikali, Ngati awa sakhala m'ngalawa inu simukhoza kupulumuka.


Ndipo popeza kulinkucha, Paulo anawachenjeza onse adye kanthu, nati, Lero ndilo tsiku lakhumi ndi chinai limene munalindira, ndi kusala chakudya, osalawa kanthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa