Machitidwe a Atumwi 27:31 - Buku Lopatulika31 Paulo anati kwa kenturiyo ndi kwa asilikali, Ngati awa sakhala m'ngalawa inu simukhoza kupulumuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Paulo anati kwa kenturiyo ndi kwa asilikali, Ngati awa sakhala m'ngalawa inu simukhoza kupulumuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Apo Paulo adauza mtsogoleri wa asilikali uja, pamodzi ndi asilikali ake omwe kuti, “Ngati anthu aŵa sakhala m'chombo muno, ndithu inu simutha kupulumuka ai.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Pamenepo Paulo anawuza wolamulira asilikali uja ndi asilikaliwo kuti, “Ngati anthu awa sakhala mʼsitima muno, inu simungapulumuke.” Onani mutuwo |