Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 27:30 - Buku Lopatulika

30 Ndipo m'mene amalinyero anafuna kuthawa m'ngalawa, natsitsira bwato m'nyanja, monga ngati anati aponye anangula kulikulu,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Ndipo m'mene amalinyero anafuna kuthawa m'ngalawa, natsitsira bwato m'nyanja, monga ngati anati aponye anangula kulikulu,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Antchito apachombo aja ankafuna kuthaŵamo m'chombo muja. Choncho adatsitsira kabwato kaja pa madzi, nachita ngati akufuna kutsitsira anangula m'nyanja kutsogolo kwa chombo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Pofuna kuthawa mʼsitimayo, oyendetsa aja anatsitsira mʼnyanja bwato lopulumukiramo nʼkumachita ngati akufuna kutsitsira anangula mʼnyanjamo kutsogolo kwa sitimayo.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 27:30
5 Mawu Ofanana  

Ndipo popita kuseri kwa chisumbu chaching'ono dzina lake Kauda, tinakhoza kumangitsa bwato koma movutika;


Koma pofika usiku wakhumi ndi chinai, potengedwa ife kwina ndi kwina m'nyanja ya Adriya, pakati pa usiku amalinyero anazindikira kuti analikuyandikira kumtunda;


Ndipo pakuopa tingatayike pamiyala, anaponya anangula anai kumakaliro, nakhumba kuti kuche.


Paulo anati kwa kenturiyo ndi kwa asilikali, Ngati awa sakhala m'ngalawa inu simukhoza kupulumuka.


Pamenepo asilikali anadula zingwe za bwato, naligwetsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa