Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 27:29 - Buku Lopatulika

29 Ndipo pakuopa tingatayike pamiyala, anaponya anangula anai kumakaliro, nakhumba kuti kuche.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Ndipo pakuopa tingatayike pamiyala, anaponya anangula anai kumakaliro, nakhumba kuti kuche.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Poopa kuti chombo chingakatsakamire pa matanthwe, adatsitsira anangula anai m'nyanja kumbuyo kwa chombo. Kenaka ankangoyembekeza molakalaka kuti kuche.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Poopa kuti tingagunde miyala, iwo anatsitsira anangula anayi mʼmadzi kumbuyo kwa sitimayo ndipo tinapemphera kuti kuche.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 27:29
8 Mawu Ofanana  

Moyo wanga uyang'anira Ambuye, koposa alonda matanda kucha; inde koposa alonda matanda kucha.


ndipo m'mene adaukweza, anachita nazo zothandizira, nakulunga ngalawa; ndipo pakuopa kuti angatayike pa Siriti, anatsitsa matanga, natengedwa motero.


Koma tiyenera kutayika pa chisumbu chakuti.


ndipo anayesa madzi, napeza mikwamba makumi awiri; ndipo katapita kanthawi, anayesanso, napeza mikwamba khumi ndi isanu.


Ndipo m'mene amalinyero anafuna kuthawa m'ngalawa, natsitsira bwato m'nyanja, monga ngati anati aponye anangula kulikulu,


M'mawa mudzati, Mwenzi atafika madzulo! Ndi madzulo mudzati, Mwezi utafika m'mawa! Chifukwa cha mantha a m'mtima mwanu amene mudzaopa nao, ndi chifukwa cha zopenya maso anu zimene mudzazipenya.


chimene tili nacho ngati nangula wa moyo, chokhazikika ndi cholimbanso, ndi chakulowa m'katikati mwa chophimba;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa