Machitidwe a Atumwi 27:28 - Buku Lopatulika28 ndipo anayesa madzi, napeza mikwamba makumi awiri; ndipo katapita kanthawi, anayesanso, napeza mikwamba khumi ndi isanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 ndipo anayesa madzi, napeza mikwamba makumi awiri; ndipo katapita kanthawi, anayesanso, napeza mikwamba khumi ndi isanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Tsono atayesa kuzama kwa nyanja, adapeza mamita 37. Atayenda pang'ono, adayesanso napeza mamita 27. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Iwo anatenga choyezera kuzama kwa nyanja ndi kupeza kuti kuzama kwake kunali mamita 36. Atayendanso pangʼono anatenganso choyezera chija napeza kuti kuzama kwake kunali 27. Onani mutuwo |