Machitidwe a Atumwi 27:27 - Buku Lopatulika27 Koma pofika usiku wakhumi ndi chinai, potengedwa ife kwina ndi kwina m'nyanja ya Adriya, pakati pa usiku amalinyero anazindikira kuti analikuyandikira kumtunda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Koma pofika usiku wakhumi ndi chinai, potengedwa ife kwina ndi kwina m'nyanja ya Adriya, pakati pa usiku amalinyero anazindikira kuti analikuyandikira kumtunda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Pakati pa usiku wa khumi ndi chinai, mphepo ikutikankhabe pa nyanja ya Adriya, antchito apachombo adaganiza kuti akuyandikira mtunda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Pakati pa usiku wa tsiku la khumi ndi chinayi tikukankhidwabe ndi mphepo mʼnyanja ya Adriya, oyendetsa sitimayo anazindikira kuti timayandikira ku mtunda. Onani mutuwo |