Machitidwe a Atumwi 27:26 - Buku Lopatulika26 Koma tiyenera kutayika pa chisumbu chakuti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Koma tiyenera kutayika pa chisumbu chakuti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Koma tidzatsakamira pa chilumba china.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Komabe tiyenera kukatsakamira pa chilumba china chake.” Onani mutuwo |