Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 27:19 - Buku Lopatulika

19 ndipo tsiku lachitatu anataya ndi manja ao a iwo eni zipangizo za ngalawa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 ndipo tsiku lachitatu anataya ndi manja ao a iwo eni zipangizo za ngalawa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Ndipo pa tsiku lachitatu lake adataya m'nyanja ndi zipangizo za chombo zomwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Pa tsiku lachitatu anaponya mʼnyanja zipangizo za mʼsitima ndi manja awo.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 27:19
7 Mawu Ofanana  

Nayankha Satana, nati kwa Yehova, Khungu kulipa khungu, inde munthu adzapereka zonse ali nazo kuombola moyo wake.


mphindi yakufunafuna ndi mphindi yakumwazika; mphindi yakusunga ndi mphindi yakutaya;


Pamenepo amalinyero anachita mantha, nafuulira yense kwa mulungu wake, naponya m'nyanja akatundu anali m'chombo kuchipepuza. Koma Yona adatsikira m'munsi mwa chombo, nagona tulo tofa nato.


Ndipo povutika kwakukulu ndi namondweyo, m'mawa mwake anayamba kutaya akatundu;


Ndipo m'mene dzuwa kapena nyenyezi sizinatiwalire masiku ambiri, ndipo namondwe wosati wamng'ono anatigwera, chiyembekezo chonse chakuti tipulumuke chidatichokera pomwepo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa