Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 27:18 - Buku Lopatulika

18 Ndipo povutika kwakukulu ndi namondweyo, m'mawa mwake anayamba kutaya akatundu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ndipo povutika kwakukulu ndi namondweyo, m'mawa mwake anayamba kutaya akatundu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Popeza kuti tinkavutika naye kwambiri namondweyo, m'maŵa mwake adayamba kutaya katundu m'madzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Ife tinavutika kwambiri ndi namondwe kotero kuti mmawa mwake tinayamba kuponya katundu mʼmadzi.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 27:18
9 Mawu Ofanana  

Adzandira napambanitsa miyendo ngati munthu woledzera, nathedwa nzeru konse.


Pamenepo amalinyero anachita mantha, nafuulira yense kwa mulungu wake, naponya m'nyanja akatundu anali m'chombo kuchipepuza. Koma Yona adatsikira m'munsi mwa chombo, nagona tulo tofa nato.


Pakuti munthu adzapindulanji, akalandira dziko lonse, nataya moyo wake? Kapena munthu adzaperekanji chosintha ndi moyo wake?


Pakuti moyo uli woposa chakudya, ndi thupi liposa chovala.


Ndipo mbuye wake anatama kapitao wonyengayo, kuti anachita mwanzeru; chifukwa ana a nthawi ya pansi pano ali anzeru m'mbadwo wao koposa ana a kuunika.


ndipo tsiku lachitatu anataya ndi manja ao a iwo eni zipangizo za ngalawa.


Ndipo m'mene anakhuta, anapepuza ngalawa, nataya tirigu m'nyanja.


Chifukwa chake ifenso, popeza tizingidwa nao mtambo waukulu wotere wa mboni, titaye cholemetsa chilichonse, ndi tchimoli limangotizinga, ndipo tithamange mwachipiriro makaniwo adatiikira, ndi kupenyerera woyambira ndi womaliza wa chikhulupiriro chathu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa