Machitidwe a Atumwi 27:17 - Buku Lopatulika17 ndipo m'mene adaukweza, anachita nazo zothandizira, nakulunga ngalawa; ndipo pakuopa kuti angatayike pa Siriti, anatsitsa matanga, natengedwa motero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 ndipo m'mene adaukweza, anachita nazo zothandizira, nakulunga ngalawa; ndipo pakuopa kuti angatayike pa Siriti, anatsitsa matanga, natengedwa motero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Kenaka adakweza kabwatoko pa chombo, ndipo pambuyo pake adakulunga chombocho ndi zingwe kuti achilimbitse. Tsono poopa kuti angakagunde ku mchenga wa ku Siriti, adatsitsa mathanga nalola kungotengedwa ndi mphepo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Anthuwo atakweza bwatolo mʼsitima, anakulunga zingwe sitimayo kuti ayilimbitse. Poopa kuti angakagunde mchenga wa ku Surti, iwo anatsitsa nangula ndi kuyilola sitima kuti idzingoyenda ndi mphepo. Onani mutuwo |