Machitidwe a Atumwi 27:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo popita kuseri kwa chisumbu chaching'ono dzina lake Kauda, tinakhoza kumangitsa bwato koma movutika; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo popita kuseri kwa chisumbu chaching'ono dzina lake Kauda, tinakhoza kumangitsa bwato koma movutika; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tidafika pafupi ndi kachilumba kotchedwa Kauda, ku mbali yosawombapo mphepo. Kumeneko movutikira tidatha kuwongolera kabwato kokokedwa ndi chombo chija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Tikudutsa mʼmbali mwa kachilumba kakangʼono kotchedwa Kawuda, tinavutika kuti tisunge bwato lopulumukiramo. Onani mutuwo |