Machitidwe a Atumwi 27:15 - Buku Lopatulika15 ndipo pogwidwa nayo ngalawa, yosakhoza kupitanso mokomana nayo mphepo, tidangoleka, ndipo tinangotengedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 ndipo pogwidwa nayo ngalawa, yosakhoza kupitanso mokomana nayo mphepo, tidangoleka, ndipo tinangotengedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Idaomba chombo chija, ndiye popeza kuti sitidathe kuchiwongolera moyang'anana ndi mphepoyo, tidaigonjera nkungotengedwa nayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mphepo yamkunthoyo inawomba sitima ija ndipo sinathe kulimbana nayo, kotero ife tinayigonjera ndi kuyamba kutengedwa nayo. Onani mutuwo |