Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 27:14 - Buku Lopatulika

14 Koma patapita pang'ono idaombetsa kuchokerako mphepo ya namondwe, yonenedwa Yurakulo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Koma patapita pang'ono idaombetsa kuchokerako mphepo ya namondwe, yonenedwa Yurakulo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Koma posachedwa mphepo yamkuntho, yotchedwa Yurakulo, idayamba kuwomba kuchokera ku mtunda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Pasanathe nthawi yayitali, mphepo yamkuntho yotchedwa Eurokulo, inayamba kuwomba kuchokera ku chilumbacho.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 27:14
7 Mawu Ofanana  

Opalasa ako anakufikitsa kumadzi aakulu; mphepo ya kum'mawa inakuthyola m'kati mwa nyanja.


Ndipo onani, panauka namondwe wamkulu panyanja, kotero kuti ngalawa inafundidwa ndi mafunde: koma Iye anali m'tulo.


Ndipo panauka namondwe wamkulu wa mphepo, ndi mafunde anagavira mungalawa, motero kuti ngalawa inayamba kudzala.


ndipo pogwidwa nayo ngalawa, yosakhoza kupitanso mokomana nayo mphepo, tidangoleka, ndipo tinangotengedwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa