Machitidwe a Atumwi 27:11 - Buku Lopatulika11 Koma kenturiyo anakhulupirira watsigiro ndi mwini ngalawa makamaka, wosasamala mau a Paulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma kenturiyo anakhulupirira watsigiro ndi mwini ngalawa makamaka, wosasamala mau a Paulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Koma mtsogoleri wa asilikali uja adamvera kapitao wa chombo ndiponso mwiniwake wa chombocho, osati mau a Paulo ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Koma wolamulira asilikali 100 uja, mʼmalo momvera zimene Paulo amanena, anatsatira malangizo a woyendetsa sitimayo ndiponso mwini wa sitimayo. Onani mutuwo |