Machitidwe a Atumwi 26:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo Agripa anati kwa Fesito, Tikadakhoza kumasula munthuyu, akadapanda kunena, Ndikatulukire kwa Kaisara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo Agripa anati kwa Fesito, Tikadakhoza kumasula munthuyu, akadapanda kunena, Ndikatulukire kwa Kaisara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Tsono Agripa adauza Fesito kuti, “Tikadammasula munthuyu akadapanda kupempha kuti mlandu wakewu ukazengedwe ndi Mfumu ya ku Roma.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Agripa anati kwa Festo, “Munthu uyu akanamasulidwa akanakhala kuti sanapemphe zokaonekera kwa Kaisara.” Onani mutuwo |