Machitidwe a Atumwi 26:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo ananyamuka mfumu, ndi kazembe, ndi Berenise, ndi iwo akukhala nao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo ananyamuka mfumu, ndi kazembe, ndi Berenise, ndi iwo akukhala nao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Pamenepo mfumu Agripa, bwanamkubwa, Berenise, ndi onse amene anali nawo adaimirira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Mfumu inayimirira pamodzi ndi bwanamkubwa ndi Bernisi ndiponso anthu onse amene anakhala nawo pamodzi. Onani mutuwo |