Machitidwe a Atumwi 26:27 - Buku Lopatulika27 Mfumu Agripa, mukhulupirira aneneri kodi? Ndidziwa kuti muwakhulupirira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Mfumu Agripa, mukhulupirira aneneri kodi? Ndidziwa kuti muwakhulupirira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Inu mfumu Agripa, kodi mumakhulupirira mau a aneneri? Ndikudziŵa kuti mumaŵakhulupirira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Mfumu Agripa, kodi mumakhulupirira mawu a aneneri? Ine ndikudziwa kuti mumakhulupirira.” Onani mutuwo |